Chifira BeachFront Lodge

Chifira BeachFront Lodge Private beachfront lodge on Lake Malawi, Chifira Nkhata-Bay— first left turn from Kapesa when coming from Mzuzu, first right after Kande Trading Bridge.
(1)

Swimming pool,Tv Sports Enter,Ice cream,Community Grocery,Executive Liquor Bar launchingAug/Nov2026.

24/08/2026

Tiyeni tizuke, Tipemphere osafooka, osatopa, osanyinyilika palibe Nyengo yosasintha abwenzi ❤️🎉 Zikomo

Tigaireni uthenga omwe mwarandira ku church kwanu lero Abwenzi 🎉🎉🎉
23/08/2026

Tigaireni uthenga omwe mwarandira ku church kwanu lero Abwenzi 🎉🎉🎉

Chifira BeachFront Lodge payokha singatheke popanda Mrs Genius 😂 ngati mwawadziwa apaseni moni mu comment box umo. Admin...
22/08/2026

Chifira BeachFront Lodge payokha singatheke popanda Mrs Genius 😂 ngati mwawadziwa apaseni moni mu comment box umo.

Admin akhara ndi ukwati 2027 January 😂😂😂

Ubwino woyamba wa page ino ndiwoti timacheza ndi aliyese ichi chikhalidwe chathu kuno ku Chifira BeachFront Lodge. Abwen...
22/08/2026

Ubwino woyamba wa page ino ndiwoti timacheza ndi aliyese ichi chikhalidwe chathu kuno ku Chifira BeachFront Lodge.

Abwenzi muli Dera liti mwina kumayenderana ❤️

Nafe taulutsa ka drone kuno Abwenzi 😂😂😂
22/08/2026

Nafe taulutsa ka drone kuno Abwenzi 😂😂😂

21/08/2026

Yohane 15 vs 7
Muwerengeko lero ndipo Ambuye akusogolereni, Zikomo Abwenzi 🎉❤️

20/08/2026

Lero timapuma ntchito inali pa KIA dzulo 🇲🇼🇲🇼🇲🇼. Abwenzi mugone bwino kumeneko 🎉

19/08/2026

Tikufuna Cooker yabwino ku Blantyre M'malo mwa Top fan wina pano, chonde ikani chithunzi ndi mtengo wake plus shop name or komwe m'mapezeka ndi Nambala yanu.

NOTE:
Zonse muike mu comment box 👇 umu not ku inbox
Zikomo.
___________________________________
Tipaseni mtengo wa fair Admin ndi mwana wanu 😂😂😂

LERO NDE ZONSE ZILIBWINO 🎉🎉🎉🎉
19/08/2026

LERO NDE ZONSE ZILIBWINO 🎉🎉🎉🎉

19/08/2026

Tiya Chitseko Congratulations 🎉🎉 Hope kafika 💰

Address

Chifira BeachFront Lodge, Chifira, Nkhata-Bay, Malawi, � First Left From Kapesa (coming From Mzuzu), � First Right After Kande Trading Bridge, Private Beachfront Along Lake
Nkhata Bay

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chifira BeachFront Lodge posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category