26/06/2026
MWAYI KWAONSE OCHITA MALONDA MUMZINDA WA MZUZU
Nthambi ya PPDA yakonza maphunziro a ulere, komwe izakuphunzitseni zamommwe mungalembetsere komanso kugulitsira katundu wanu kuboma kudzera pa ndondomeko yatsopano ya pamakina a intaneti ya MANePS.
Kaya mumaperekera stationery, zakudya, katundu okhudza magalimoto, zaulimi mwazina; maphunzirowa ndi anu.
MALO: Illala Crest Lodge
Nthawi: 8:30am
JAMBULANI QR CODE KAPENA DINANI LINK YOTSATIRAYI KUTI MULEMBETSE.
https://forms.office.com/r/gn3NmwdXa4